Levitiko 13:14 - Buku Lopatulika14 Koma tsiku lililonse ukaoneka pa iye mnofu wofiira, adzakhala wodetsedwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Koma tsiku lililonse ukaoneka pa iye mnofu wofiira, adzakhala wodetsedwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Koma pathupi pake pakaoneka zilonda, ndiye kuti munthuyo ndi woipitsidwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Koma pa tsiku limene zilonda zidzaoneka pa iye, munthuyo adzakhala wodetsedwa. Onani mutuwo |