Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Levitiko 13:13 - Buku Lopatulika

13 pamenepo wansembe aone, ndipo taonani, ngati khate lakuta thupi lake, amutche woyera wanthendayo; patuwa ponsepo; ndiye woyera.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 pamenepo wansembe aone, ndipo taonani, ngati khate lakuta thupi lake, amutche woyera wanthendayo; patuwa ponsepo; ndiye woyera.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 pamenepo wansembeyo aonetsetse. Khatelo likakhala litagwira thupi lonse, wodwalayo amutchule kuti ndi wosaipitsidwa. Thupi lonse lasanduka loyera ndipo munthuyo ndi wosaipitsidwa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 wansembe amuonetsetse munthuyo, ndipo ngati khatero lagwira thupi lake lonse, wansembe alengeze kuti munthuyo ndi woyera. Popeza kuti thupi lonse lasanduka loyera, munthuyo ndi woyeretsedwa.

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 13:13
6 Mawu Ofanana  

Pakuti ife tonse takhala ngati wina amene ali wosakonzeka; ndi zolungama zathu zonse zili ngati chovala chodetsedwa; ndipo ife tonse tifota monga tsamba, ndi zoipa zathu zitiuluza monga mphepo.


Ndipo ngati khate libukabuka pakhungu, ndi khate lakuta khungu lonse la wanthendayo kuyambira mutu wake kufikira mapazi ake, monga momwe apenyera wansembe;


Koma tsiku lililonse ukaoneka pa iye mnofu wofiira, adzakhala wodetsedwa.


Ndipo mtambo unachoka pachihema; ndipo taonani, Miriyamu anali wakhate, wa mbuu ngati chipale chofewa; ndipo Aroni anapenya Miriyamu, taonani, anali wakhate.


Yesu anati kwa iwo, Mukadakhala osaona simukadakhala nalo tchimo; koma tsopano munena, kuti, Tipenya: tchimo lanu likhala.


Chenjerani nayo nthenda yakhate, kusamaliratu, ndi kuchita monga mwa zonse akuphunzitsani ansembe Alevi; monga ndinalamulira iwo, momwemo muzisamalira kuchita.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa