Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Levitiko 13:12 - Buku Lopatulika

12 Ndipo ngati khate libukabuka pakhungu, ndi khate lakuta khungu lonse la wanthendayo kuyambira mutu wake kufikira mapazi ake, monga momwe apenyera wansembe;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Ndipo ngati khate libukabuka pakhungu, ndi khate lakuta khungu lonse la wanthendayo kuyambira mutu wake kufikira mapazi ake, monga momwe apenyera wansembe;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Khatelo likafalikira pa khungu, kotero kuti likhala litagwira khungu lonse la munthu wodwalayo kuyambira kumutu mpaka kumapazi, monga m'mene wansembe angaonere,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 “Ndipo ngati, mʼkuona kwa wansembe, khate lija lafalikira pa khungu lonse moti lamugwira thupi lonse kuyambira kumutu mpaka kumapazi,

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 13:12
9 Mawu Ofanana  

tsono pempho ndi pembedzero lililonse akalipempha munthu aliyense, kapena anthu anu onse Aisraele, pakuzindikira munthu yense chinthenda cha mtima wa iye yekha, ndi kutambasulira manja ake kunyumba ino;


Taonani, ndakhululuka ine, ndidzakubwezerani mau otani? Ndigwira pakamwa.


chifukwa chake ndekha ndidzinyansa, ndi kulapa m'fumbi ndi mapulusa.


Pakuti ife tonse takhala ngati wina amene ali wosakonzeka; ndi zolungama zathu zonse zili ngati chovala chodetsedwa; ndipo ife tonse tifota monga tsamba, ndi zoipa zathu zitiuluza monga mphepo.


ndilo khate lakale pa khungu la thupi lake, ndipo wansembe amutche wodetsedwa; asambindikiretse popeza ali wodetsedwa.


pamenepo wansembe aone, ndipo taonani, ngati khate lakuta thupi lake, amutche woyera wanthendayo; patuwa ponsepo; ndiye woyera.


Pakuti tidziwa kuti chilamulo chili chauzimu; koma ine ndili wathupi, wogulitsidwa kapolo wa uchimo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa