Levitiko 13:11 - Buku Lopatulika11 ndilo khate lakale pa khungu la thupi lake, ndipo wansembe amutche wodetsedwa; asambindikiretse popeza ali wodetsedwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 ndilo khate lakale pa khungu la thupi lake, ndipo wansembe amutche wodetsedwa; asambindikiretse popeza ali wodetsedwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 limenelo ndi khate lachikhalire limene lili pakhungu pakelo, ndipo wansembe amutchule kuti ndi woipitsidwa. Sikufunika kumtsekera chifukwa ndi woipitsidwadi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 limenelo ndi khate lachikhalire la pa khungu, ndipo wansembe alengeze kuti munthuyo ndi wodetsedwa. Asamutsekere munthu woteroyo pakuti ndi wodetsedwa kale. Onani mutuwo |