Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Levitiko 11:6 - Buku Lopatulika

6 Ndi kalulu, popeza abzikula koma wosagawanika chiboda, mumuyese wodetsedwa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Ndi kalulu, popeza abzikula koma wosagawanika chiboda, mumuyese wodetsedwa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Kalulu: ameneyu ndi wonyansa kwa inu, chifukwa ngakhale amabzikula, ziboda zake nzosagaŵikana.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Inanso ndi kalulu, ngakhale amabzikula, zipondero zake nʼzosagawikana. Choncho ndi wodetsedwa, musadye.

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 11:6
4 Mawu Ofanana  

Nyama iliyonse yogawanika chiboda, nikhala yogawanikadi chiboda, ndi yobzikula, imeneyo muyenera kudya.


Ndi mbira, ingakhale ibzikula koma yosagawanika chiboda, muiyese yodetsedwa.


Ndi nkhumba, popeza igawanika chiboda, nikhala yogawanikadi chiboda, koma yosabzikula, muiyese yodetsedwa.


Koma izi zokha simuyenera kuzidya mwa zobzikulazo, kapena zogawanika chiboda: ngamira, ndi kalulu, ndi mbira, popeza zibzikula, koma zosagawanika chiboda, muziyese zodetsa;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa