Levitiko 11:5 - Buku Lopatulika5 Ndi mbira, ingakhale ibzikula koma yosagawanika chiboda, muiyese yodetsedwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndi mbira, ingakhale ibzikula koma yosagawanika chiboda, muiyese yodetsedwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Mbira: imeneyi njonyansa kwa inu, chifukwa ngakhale imabzikula, ziboda zake nzosagaŵikana. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Ina ndi mbira, ngakhale imabzikula, zipondero zake nʼzosagawikana. Choncho ndi yodetsedwa, musadye. Onani mutuwo |