Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Levitiko 11:41 - Buku Lopatulika

41 Ndipo zokwawa zonse zakukwawa padziko lapansi zikhale zonyansa; musamazidya.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

41 Ndipo zokwawa zonse zakukwawa pa dziko lapansi zikhale zonyansa; musamazidya.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

41 “Chinthu chilichonse chokwaŵa pansi nchonyansa, ndipo musadye.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

41 “ ‘Chinthu chilichonse chokwawa pansi ndi chonyansa, simuyenera kudya.

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 11:41
6 Mawu Ofanana  

Ndipo anati Mulungu, Madzi abale zochuluka zamoyo zoyendayenda, ndi mbalame ziuluke pamwamba padziko lapansi ndi pamlengalenga.


Ndipo zinafa zamoyo zonse zoyenda padziko lapansi, zouluka, ndi nyama, ndi zamoyo, ndi zokwawa zonse zakukwawa padziko lapansi, ndi anthu onse:


Zokwawa zonse zakuuluka zokhala ndi miyendo inai, muziyesa izi zonyansa.


Koma zokwawa zonse zakuuluka, za miyendo inai, muziyese zonyansa.


Ndipo izi ndi zimene muziziyesa zodetsedwa mwa zinthu zokwawa zakukwawa pansi; likongwe, ndi mbewa, ndi msambulu mwa mtundu wake;


Zonse zoyenda chafufumimba, ndi zonse za miyendo inai, kapena zonse zokhala nayo miyendo yambiri ndi zokwawa zonse zakukwawa pansi, musamazidya; popeza ndizo zonyansa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa