Levitiko 11:34 - Buku Lopatulika34 Chakudya chilichonse chokhala m'mwemo, chokonzeka ndi madzi, chidzakhala chodetsedwa; ndi chakumwa chilichonse m'chotengera chotere chidzakhala chodetsedwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Chakudya chilichonse chokhala m'mwemo, chokonzeka ndi madzi, chidzakhala chodetsedwa; ndi chakumwa chilichonse m'chotengera chotere chidzakhala chodetsedwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Madzi am'mbiyamo akathira pa chakudya chilichonse, chakudyacho chidzakhala chonyansa. Chakumwa chilichonse cha m'mbiya ya mtundu umenewo chidzakhala chonyansa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Chakudya chilichonse chimene mungadye chikakhala kuti chathiridwa mʼmbiyamo, ndiye kuti chakudyacho chidzakhala chodetsedwa, ndipo madzi akumwa wochokera mʼmbiya zotere ndi wodetsedwa. Onani mutuwo |