Levitiko 11:16 - Buku Lopatulika16 ndi nthiwatiwa, ndi chipudo, ndi kakowa, ndi kabawi mwa mtundu wake; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 ndi nthiwatiwa, ndi chipudo, ndi kakowa, ndi kabawi mwa mtundu wake; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 nthiŵatiŵa, chipudo, kakoŵa, akabaŵi a mitundu yonse, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 kadzidzi wamphondo, kadzidzi wodzuma, chipudo ndi mtundu uliwonse wa akabawi Onani mutuwo |