Levitiko 11:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo mwa mbalame muziziyesa zonyansa izi; simuyenera kuzidya, zonyansa ndi izi: mphungu, ndi nkhwazi, ndi chikambi; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo mwa mbalame muziziyesa zonyansa izi; siziyenera kuzidya, zonyansa ndi izi: mphungu, ndi nkhwazi, ndi chikambi; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 “Ndipo mbalame zimene muyenera kuziyesa zonyansa, zoti simuyenera kudya, popeza kuti nzonyansa kwa inu, ndi izi: mphungu, nkhwazi, ndi muimba, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 “ ‘Mbalame zimene simukuyenera kudya chifukwa ndi zodetsedwa ndi izi: mphungu, nkhwazi, mwimba, Onani mutuwo |