Levitiko 11:12 - Buku Lopatulika12 Zilizonse zopanda zipsepse kapena mamba m'madzimo muziyese zonyansa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Zilizonse zopanda zipsepse kapena mamba m'madzimo muziyese zonyansa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Zamoyo zonse zam'madzi zopanda zilimba ndi mamba, nzonyansa kwa inu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Chamoyo chilichonse cha mʼmadzi chimene chilibe minga ya pa msana kapena mamba ndi chodetsedwa kwa inu. Onani mutuwo |