Levitiko 10:5 - Buku Lopatulika5 Pamenepo anasendera pafupi, nawanyamula osawavula malaya ao a m'kati, kunka nao kunja kwa chigono, monga Mose adauza. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Pamenepo anasendera pafupi, nawanyamula osawavula malaya ao a m'kati, kunka nao kunja kwa chigono, monga Mose adauza. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Iwo adasenderadi pafupi, naŵanyamula ali ndi mikanjo yao ndi kuŵatulutsira kunja kwa mahema, monga momwe Mose adaŵauzira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Choncho anabwera atavala minjiro yawo ndipo anawatenga ndi kuwatulutsa kunja kwa msasawo monga momwe Mose analamulira. Onani mutuwo |