Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Levitiko 10:18 - Buku Lopatulika

18 Taonani, sanalowe nao mwazi wake m'malo opatulika m'katimo; mukadaidyera ndithu m'malo opatulika, monga ndinakuuzani.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

18 Taonani, sanalowe nao mwazi wake m'malo opatulika m'katimo; mukadaidyera ndithu m'malo opatulika, monga ndinakuuzani.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

18 Chifukwa magazi ake sadaloŵe nawo m'katikati mwa malo oyera kwambiri, mukadayenera kudyera zimenezi pa malo oyera, monga momwe ndidalamulira.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

18 Pakuti magazi ake sanalowe nawo ku Malo Wopatulika, mukanadya nyama ya mbuziyo pa malo wopatulikawo monga Yehova analamulira.”

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 10:18
4 Mawu Ofanana  

Ndipo adye zimene anachita nazo choteteza, kuti awadzaze manja ndi kuwapatulitsa; koma mlendo asadyeko, pakuti nzopatulika izi.


Ndipo Yehova analankhula ndi Mose, nati,


Ndipo azidya iyi wansembe amene aipereka chifukwa cha zoipa; aidyere m'malo opatulika, pa bwalo la chihema chokomanako.


Koma asadye nsembe yauchimo iliyonse, imene amadza nao mwazi wake ku chihema chokomanako kutetezera nao m'malo opatulika; aitenthe ndi moto.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa