Levitiko 10:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo Mose anafunafuna mbuzi ya nsembe yauchimo, ndipo taonani, adaitentha. Ndipo anapsa mtima pa Eleazara ndi Itamara, ana otsalawo a Aroni, nati, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo Mose anafunafuna mbuzi ya nsembe yauchimo, ndipo taonani, adaitentha. Ndipo anapsa mtima pa Eleazara ndi Itamara, ana otsalawo a Aroni, nati, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Tsono Mose adafunafuna mbuzi ya nsembe yopepesera machimo, ndipo adapeza kuti adaitentha kale. Ndipo adakalipira Eleazara ndi Itamara, ana a Aroni otsala aja. Adati, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Pambuyo pake Mose anafunafuna mbuzi ya nsembe yopepesera machimo koma anapeza kuti anayitentha kale. Apa Mose anakalipira Eliezara ndi Itamara, ana a Aaroni otsala aja nati, Onani mutuwo |