Hoseya 9:14 - Buku Lopatulika14 Apatseni, Yehova; mudzapatsa chiyani? Muwapatse mimba yotayataya, ndi mawere ouma. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Apatseni, Yehova; mudzapatsa chiyani? Muwapatse mimba yotayataya, ndi mawere ouma. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Muŵapatse, Inu Chauta. Kodi mudzaŵapatse chiyani? Muŵapatse mimba yopita padera ndi maŵere ouma! Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Inu Yehova, muwapatse. Kodi mudzawapatsa chiyani? Apatseni mimba yomangopita padera ndi mawere owuma. Onani mutuwo |