Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Hagai 2:8 - Buku Lopatulika

8 Siliva ndi wanga, golide ndi wanga, ati Yehova wa makamu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Siliva ndi wanga, ya golide ndi wanga, ati Yehova wa makamu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Siliva yense ndi wanga, golide yense ndi wanga.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 ‘Siliva yense ndi wanga, golide yense ndi wanganso,’ akutero Yehova Wamphamvuzonse.

Onani mutuwo Koperani




Hagai 2:8
7 Mawu Ofanana  

Kodi idzachulukitsa mau akukupembedza? Kapena idzanena nawe mau ofatsa?


Dziko lapansi nla Yehova ndi zodzala zake zomwe, dziko lokhalamo anthu ndi iwo okhala m'mwemo.


Ulemerero wa Lebanoni udzafika kwa iwe; mtengo wamlombwa, mtengo wamkuyu ndi mtengo wanaphini pamodzi, kukometsera malo a Kachisi wanga; ndipo ndidzachititsa malo a mapazi anga ulemerero.


M'malo mwa mkuwa ndidzatenga golide, ndi m'malo mwa chitsulo ndidzatenga siliva, ndi m'malo mwa mtengo ndidzatenga mkuwa, ndi m'malo mwa miyala ndidzatenga chitsulo; ndidzakuikira akapitao a mtendere, ndi oyang'anira ntchito a chilungamo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa