Genesis 46:31 - Buku Lopatulika31 Ndipo Yosefe anati kwa abale ake, ndi kwa mbumba ya atate wake, Ndidzanka, ndikauze Farao, ndipo ndidzati kwa iye, Abale anga ndi mbumba ya atate wanga, amene anali m'dziko la Kanani, afika kwa ine; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Ndipo Yosefe anati kwa abale ake, ndi kwa mbumba ya atate wake, Ndidzanka, ndikauze Farao, ndipo ndidzati kwa iye, Abale anga ndi mbumba ya atate wanga, amene anali m'dziko la Kanani, afika kwa ine; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 Apo Yosefe adauza abale ake aja pamodzi ndi banja lonse la bambo wake kuti “Ndipita ndikamuuze Farao kuti abale anga pamodzi ndi onse a m'banja la atate anga amene ankakhala ku Kanani, abwera kuno kwa ine. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 Ndipo Yosefe anati kwa abale ake pamodzi ndi a pa banja la abambo ake, “Ndipita kwa Farao ndipo ndikamuwuza kuti, ‘Abale anga pamodzi ndi onse a mʼnyumba ya abambo anga amene amakhala mʼdziko la Kanaani abwera kuno kwa ine. Onani mutuwo |