Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Genesis 46:30 - Buku Lopatulika

30 Ndipo Israele anati kwa Yosefe, Ndife tsopano, popeza ndaona nkhope yako, kuti ukali ndi moyo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

30 Ndipo Israele anati kwa Yosefe, Ndife tsopano, popeza ndaona nkhope yako, kuti ukali ndi moyo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

30 Israele adauza Yosefe kuti, “Tsopano ndimwalire, popeza kuti ndakuwona, ndipo ndikudziŵadi kuti uli moyo.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

30 Israeli anati kwa Yosefe, “Tsopano ndikhoza kumwalira poti ndaona nkhope yako kuti ukanali ndi moyo.”

Onani mutuwo Koperani




Genesis 46:30
4 Mawu Ofanana  

ndipo Israele anati, Chakwana; Yosefe mwana wanga akali ndi moyo; ndidzamuka ndikamuone iye ndisanafe.


Ndipo Yosefe anamanga galeta lake nakwera kunka kukakomana naye Israele atate wake, ku Goseni, ndipo anadzionetsera yekha kwa iye, nagwera pakhosi pake nakhala m'kulira pakhosi pake.


Ndipo Yosefe anati kwa abale ake, ndi kwa mbumba ya atate wake, Ndidzanka, ndikauze Farao, ndipo ndidzati kwa iye, Abale anga ndi mbumba ya atate wanga, amene anali m'dziko la Kanani, afika kwa ine;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa