Genesis 46:29 - Buku Lopatulika29 Ndipo Yosefe anamanga galeta lake nakwera kunka kukakomana naye Israele atate wake, ku Goseni, ndipo anadzionetsera yekha kwa iye, nagwera pakhosi pake nakhala m'kulira pakhosi pake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 Ndipo Yosefe anamanga galeta lake nakwera kunka kukakomana naye Israele atate wake, ku Goseni, ndipo anadzionetsera yekha kwa iye, nagwera pakhosi pake nakhala m'kulira pakhosi pake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 Yosefe adaitanitsa galeta lake, napita ku Goseni kukakumana ndi Israele bambo wake. Atangofika pamaso pake, adamkumbatira m'khosi, nalira nthaŵi yaitali ndithu, osalekerapo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Yosefe anakonza galeta nakwerapo ndi kupita ku Goseni kukakumana ndi abambo ake, Israeli. Yosefe atangofika pamaso pa abambo ake, anawakumbatira nalira kwa nthawi yayitali. Onani mutuwo |