Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Genesis 46:23 - Buku Lopatulika

23 Ndi ana aamuna a Dani: Husimu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

23 Ndi ana amuna a Dani: Husimu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

23 Dani anali ndi mwana mmodzi yekha dzina lake Husimu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

23 Mwana wa mwamuna wa Dani anali: Husimu.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 46:23
13 Mawu Ofanana  

Rakele ndipo anati, Mulungu wandiweruzira ine, namva mau anga, nandipatsa ine mwana; chifukwa chake anamutcha dzina lake Dani.


ana aamuna a Biliha mdzakazi wake wa Rakele: ndiwo Dani ndi Nafutali;


Amenewo ndi ana a Rakele, amene anabadwira Yakobo; anthu onse ndiwo khumi ndi anai.


Ndi ana aamuna a Nafutali: Yazeele, ndi Guni, ndi Yezere ndi Silemu.


Ndi a Adani akupangira nkhondo zikwi makumi awiri mphambu zisanu ndi zitatu kudza mazana asanu ndi limodzi.


Dani, Yosefe, ndi Benjamini, Nafutali, Gadi, ndi Asere.


Supimu yemwe ndi Hupimu ana a Iri, ndi Husimu mwana wa Aheri.


Wa Dani, Ahiyezere mwana wa Amisadai.


Pamenepo anayenda a mbendera ya chigono cha ana a Dani, ndiwo a m'mbuyombuyo a zigono zonse, monga mwa magulu ao; ndi pa gulu lake anayang'anira Ahiyezere mwana wa Amisadai.


Ndi za Dani anati, Dani ndiye mwana wa mkango, wakutumpha motuluka mu Basani.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa