Genesis 46:22 - Buku Lopatulika22 Amenewo ndi ana a Rakele, amene anabadwira Yakobo; anthu onse ndiwo khumi ndi anai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Amenewo ndi ana a Rakele, amene anabadwira Yakobo; anthu onse ndiwo khumi ndi anai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 (Onseŵa 14 ndiwo adzukulu a Yakobe mwa mkazi wake Rakele.) Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Amenewa ndi zidzukulu za Yakobo mwa mkazi wake Rakele. Onse analipo khumi ndi anayi. Onani mutuwo |