Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Genesis 46:21 - Buku Lopatulika

21 Ndi ana aamuna a Benjamini: Bela ndi Bekere, ndi Asibele, ndi Gera, ndi Naamani, ndi Ehi ndi Rosi, Mupimu ndi Hupimu, ndi Aridi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

21 Ndi ana amuna a Benjamini: Bela ndi Bekere, ndi Asibele, ndi Gera, ndi Naamani, ndi Ehi ndi Rosi, Mupimu ndi Hupimu, ndi Aridi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

21 Ana a Benjamini anali aŵa: Bela, Bekara, Asibele, Gera, Naamani, Ehi, Rosi, Mupimu, Hupimu ndi Aridi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

21 Ana aamuna a Benjamini ndi awa: Bela, Bekeri, Asibeli, Gera, Naamani, Ehi, Rosi, Mupimu, Hupimu ndi Aridi.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 46:21
9 Mawu Ofanana  

Amenewo ndi ana a Rakele, amene anabadwira Yakobo; anthu onse ndiwo khumi ndi anai.


Benjamini ndiye mmbulu wakulusalusa; m'mamawa adzadya chomotola, madzulo adzagawa zofunkha.


Ndipo kudangotero kuti pamenepo panali munthu woipa, dzina lake ndiye Sheba mwana wa Bikiri Mbenjamini; naliza iye lipenga, nati, Ife tilibe gawo mwa Davide, tilibenso cholowa mwa mwana wa Yese; munthu yense apite ku mahema ake, Israele inu.


Wa Benjamini, Abidani mwana wa Gideoni.


Za Benjamini anati, Wokondedwa wa Yehova adzakhala ndi Iye mokhazikika; am'phimba tsiku lonse, inde akhalitsa pakati pa mapewa ake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa