Genesis 46:14 - Buku Lopatulika14 Ndi ana aamuna a Zebuloni: Seredi, ndi Eloni ndi Yaleele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndi ana amuna a Zebuloni: Seredi, ndi Eloni ndi Yaleele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Ana a Zebuloni anali aŵa: Seredi, Eloni ndi Yaleele. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Ana aamuna a Zebuloni ndi awa: Seredi, Eloni ndi Yahaleeli. Onani mutuwo |