Genesis 45:28 - Buku Lopatulika28 ndipo Israele anati, Chakwana; Yosefe mwana wanga akali ndi moyo; ndidzamuka ndikamuone iye ndisanafe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 ndipo Israele anati, Chakwana; Yosefe mwana wanga akali ndi moyo; ndidzamuka ndikamuone iye ndisanafe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 Tsono adati, “Basi chabwino, mwana wanga Yosefe akali moyo. Ndipita ndikamuwone ndisanafe.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 Ndipo Israeli anati, “Ndatsimikizadi! Mwana wanga Yosefe akanali ndi moyodi. Ndipita ndikamuone ndisanafe.” Onani mutuwo |