Genesis 44:32 - Buku Lopatulika32 Pakuti kapolo wanu anadziyesa chikole cha mnyamata pa atate wanga, kuti, Ndikapanda kumbwezeranso kwa inu, pamenepo ndidzakhala ndi chifukwa kwa atate wanga nthawi zonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201432 Pakuti kapolo wanu anadziyesa chikole cha mnyamata pa atate wanga, kuti, Ndikapanda kumbwezeranso kwa inu, pamenepo ndidzakhala ndi chifukwa kwa atate wanga nthawi zonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa32 Ndiponsotu bwana, ine ndidapereka moyo wanga kwa bambo wanga chifukwa cha mnyamata ameneyu. Ndidamuuza kuti ngati mnyamatayu sindidzabwerera naye, ndidzakhala wolakwa pamaso pa bambo wanga moyo wanga onse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero32 Ndiponsotu ine ndinadzipereka kwa abambo anga kukhala chikole chotsimikiza kuti mnyamatayu ndidzamuteteza, ndipo ndinati, ‘Ngati sindibwerera naye mnyamatayu kwa inu, ndiye kuti ndidzakhala wochimwira inu abambo anga moyo wanga wonse.’ Onani mutuwo |