Genesis 44:29 - Buku Lopatulika29 ndipo ngati mukandichotsera ameneyonso, ndipo ngati chimgwera choipa, mudzanditsitsira ndi chisoni imvi zanga kumanda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 ndipo ngati mukandichotsera ameneyonso, ndipo ngati chimgwera choipa, mudzanditsitsira ndi chisoni imvi zanga kumanda. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 Tsopano mukanditengeranso uyu, nakaphedwa, ndiye kuti ine ndidzafa ndi chisoni.’ ” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Tsopano mukanditengeranso uyu, nakaphedwa mu njira ndiye kuti mudzandikankhira ku manda ndi chisoni.’ Onani mutuwo |