Genesis 44:26 - Buku Lopatulika26 Ndipo ife tinati, Sitingathe kupita; mphwathu wamng'ono akakhala ndi ife, pamenepo tidzapita; pakuti sitingaone nkhope ya munthu uja, mphwathu wamng'ono akapanda kukhala ndi ife. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Ndipo ife tinati, Sitingathe kupita; mphwathu wamng'ono akakhala ndi ife, pamenepo tidzapita; pakuti sitingaone nkhope ya munthu uja, mphwathu wamng'ono akapanda kukhala ndi ife. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 ife tidamuuza bambo wathu kuti, ‘Sitingathe kupita popeza kuti munthu uja sakatilola kufika pamaso pake, tikapanda kupita ndi mng'ono wathuyu.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Koma tinati, ‘Sitingathe kupitanso. Sitingapite pokhapokha mngʼono wathuyu apite nafe chifukwa munthu uja anati sitingaonane naye ngati mngʼono wathuyu sakhala nafe.’ Onani mutuwo |