Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Genesis 44:25 - Buku Lopatulika

25 Ndipo atate wathu anati, Mupitenso mutigulire ife chakudya pang'ono.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

25 Ndipo atate wathu anati, Mupitenso mutigulire ife chakudya pang'ono.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

25 Iye atatiwuza kuti, ‘Bwererani mukatigulireko chakudya pang'ono,’

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

25 “Abambo athu anatiwuza kuti, ‘Pitaninso mukagule kachakudya pangʼono.’

Onani mutuwo Koperani




Genesis 44:25
4 Mawu Ofanana  

Ndipo panali pamene atatha kudya tirigu yense anatengayo ku Ejipito atate wao anati kwa iwo, Pitaninso, mukatigulire ife chakudya pang'ono.


Koma mukapanda kumtuma iye sititsika; pakuti munthu uja anati kwa ife, Simudzaona nkhope yanga, ngati mphwanu sali ndi inu.


Ndipo panali titakwera kunka kwa kapolo wanu atate wanga, tinamfotokozera iye mau a mbuyanga.


Ndipo ife tinati, Sitingathe kupita; mphwathu wamng'ono akakhala ndi ife, pamenepo tidzapita; pakuti sitingaone nkhope ya munthu uja, mphwathu wamng'ono akapanda kukhala ndi ife.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa