Genesis 44:24 - Buku Lopatulika24 Ndipo panali titakwera kunka kwa kapolo wanu atate wanga, tinamfotokozera iye mau a mbuyanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Ndipo panali titakwera kunka kwa kapolo wanu atate wanga, tinamfotokozera iye mau a mbuyanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Titabwerera kwathu kwa bambo wathu mtumiki wanu, tidamuuza mau anu onse aja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Ndiye pamene tinafika kwa kapolo wanu, abambo athu tinawawuza zonse zimene munanena. Onani mutuwo |