Genesis 44:23 - Buku Lopatulika23 Ndipo munati kwa akapolo anu, Koma ngati mbale wanu safika pamodzi ndi inu, simudzaonanso konse nkhope yanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ndipo munati kwa akapolo anu, Koma ngati mbale wanu safika pamodzi ndi inu, simudzaonanso konse nkhope yanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Tsono paja mudaanena kuti simudzatilola kufikanso pamaso panu tikadzapanda kubwera naye mng'ono wathuyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Koma inu munatichenjeza kuti, ‘Pokhapokha mutabwera naye mʼbale wanu wamngʼono kwambiri, simudzandionanso.’ Onani mutuwo |