Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Genesis 44:22 - Buku Lopatulika

22 Ndipo ife tinati kwa mbuyanga, Mnyamata sangathei kumsiya atate wake; pakuti akamsiya atate wake, atate wake adzafa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

22 Ndipo ife tinati kwa mbuyanga, Mnyamata sangathei kumsiya atate wake; pakuti akamsiya atate wake, atate wake adzafa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

22 Ife tidaakuyankhani kuti, ‘Mnyamatayo sangachoke kwa bambo wake, popeza kuti akatero, bambo wakeyo kufa kudzakhala komweko.’

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

22 Ife tinati, ‘Mbuye wathu, mnyamatayo sangasiye abambo ake, akawasiya ndiye kuti abambo akewo adzafa.’

Onani mutuwo Koperani




Genesis 44:22
4 Mawu Ofanana  

Ndipo iye anati, Mwana wanga sadzatsikira ndi inu, chifukwa kuti mkulu wake wafa, ndipo watsala iye yekha; ngati choipa chikamgwera iye m'njira m'mene mupitamo, inu mudzatsitsira ndi chisoni imvi zanga kumanda.


Ndipo munati kwa akapolo anu, Munditengere iye, kuti ndimuone iye m'maso mwanga.


Ndipo munati kwa akapolo anu, Koma ngati mbale wanu safika pamodzi ndi inu, simudzaonanso konse nkhope yanga.


Chifukwa chake ndikafika kwa kapolo wanu atate wanga, ndipo mnyamata akapanda kukhala ndi ife; popeza moyo wanu uli womangidwa ndi moyo wa mnyamatayo;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa