Genesis 44:15 - Buku Lopatulika15 Ndipo Yosefe anati kwa iwo, Ichi nchiyani mwachichita? Kodi simudziwa kuti munthu ngati ine ndingathe kuzindikira ndithu? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndipo Yosefe anati kwa iwo, Ichi nchiyani mwachichita? Kodi simudziwa kuti munthu ngati ine ndingathe kuzindikira ndithu? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Yosefe adati, “Mwachita chiyani? Kodi simukudziŵa kuti munthu monga ine ndingathe kudziŵa zakutsogolo?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Yosefe anafunsa kuti, “Nʼchiyani mwachitachi? Kodi simudziwa kuti munthu ngati ine ndikhoza kuona zinthu mwakuwombeza?” Onani mutuwo |