Genesis 43:33 - Buku Lopatulika33 Ndipo anakhala pamaso pake, woyamba monga ukulu wake, ndi wamng'ono monga ung'ono wake; ndipo anazizwa wina ndi wina. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201433 Ndipo anakhala pamaso pake, woyamba monga ukulu wake, ndi wamng'ono monga ung'ono wake; ndipo anazizwa wina ndi wina. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa33 Abalewo adaakhala pa tebulo patsogolo pa Yosefe, ndipo anali ataŵaika motsatana ndi kubadwa kwao, kuyambira wamkulu mpaka wamng'ono. Abale aja ataona m'mene aŵakhazikira, adadabwa kwambiri namapenyetsetsana. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero33 Abale aja anawakhazika patsogolo pa Yosefe. Iwo anawakhazika monga mwa mabadwidwe awo kuyambira woyamba kubadwa mpaka wotsirizira; ndipo ankangoyangʼanitsitsana modabwa. Onani mutuwo |