Genesis 43:20 - Buku Lopatulika20 Mfumu, tinatsikira ndithu nthawi yoyamba kudzagula chakudya: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Mfumu, tinatsikira ndithu nthawi yoyamba kudzagula chakudya: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 namuuza kuti, “Pepani bwana, ife tidaabweranso kuno kale kudzagula chakudya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 “Pepani mbuye wathu, ife tinabweranso ulendo woyamba kudzagula chakudya Onani mutuwo |