Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Genesis 36:40 - Buku Lopatulika

40 Maina a mafumu obadwa kwa Esau, monga mabanja ao, monga malo ao, monga maina ao ndi awa: mfumu Timna, mfumu Aliva, mfumu Yeteti,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

40 Maina a mafumu obadwa kwa Esau, monga mabanja ao, monga malo ao, monga maina ao ndi awa: mfumu Timna, mfumu Aliva, mfumu Yeteti:

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

40 Aŵa ndiwo mafumu a kubanja kwa Esau mwatsatanetsatane, malinga ndi mafuko ao ndi malo a fuko lililonse: Timna, Aliva, Yeteti,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

40 Mayina a mafumu ochokera mwa zidzukulu za Esau malingana ndi mafuko awo ndi malo a fuko lililonse anali awa: Timna, Aliva, Yeteti,

Onani mutuwo Koperani




Genesis 36:40
6 Mawu Ofanana  

Amenewa ndi mafumu analamulira m'dziko la Edomu, asadalamulire ana a Israele mfumu aliyense.


Ndipo Baala-Hanani mwana wamwamuna wa Akibori anamwalira, ndipo Hadari analamulira m'malo mwake; dzina la mzinda wake ndi Pau; ndipo dzina la mkazi wake ndi Mehetabele, mwana wamkazi wa Matiredi, mwana wamkazi wa Mezahabu.


mfumu Oholibama, mfumu Ela, mfumu Pinoni,


Pamenepo mafumu a Edomu anadabwa; agwidwa nako kunthunthumira amphamvu a ku Mowabu; okhala mu Kanani onse asungunuka mtima.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa