Genesis 36:39 - Buku Lopatulika39 Ndipo Baala-Hanani mwana wamwamuna wa Akibori anamwalira, ndipo Hadari analamulira m'malo mwake; dzina la mzinda wake ndi Pau; ndipo dzina la mkazi wake ndi Mehetabele, mwana wamkazi wa Matiredi, mwana wamkazi wa Mezahabu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201439 Ndipo Baala-Hanani mwana wamwamuna wa Akibori anamwalira, ndipo Hadari analamulira m'malo mwake; dzina la mudzi wake ndi Pau; ndipo dzina la mkazi wake ndi Mehetabele, mwana wamkazi wa Matiredi, mwana wamkazi wa Mezahabu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa39 Baala-Hanani mwana wa Akibori atafa, Hadari ndiye adaloŵa ufumu m'malo mwake. Dzina la mzinda wake linali Pau, ndipo dzina la mkazi wake linali Mehetabele, mwana wa Matiredi mwana wa Mezahabu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero39 Pamene Baala-Hanani mwana wa Akibori anamwalira, Hadari analowa ufumu mʼmalo mwake. Mzinda wake unkatchedwa Pau, ndipo dzina la mkazi wake linali Mehatabeli, mwana wamkazi wa Matiredi, mwana wamkazi wa Me-Zahabu. Onani mutuwo |