Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Genesis 36:36 - Buku Lopatulika

36 Ndipo Hadadi anamwalira, ndipo Samila wa ku Masireka analamulira m'malo mwake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

36 Ndipo Hadadi anamwalira, ndipo Samila wa ku Masireka analamulira m'malo mwake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

36 Atafa Hadadi, Samila wa ku Masireka ndiye adaloŵa ufumu m'malo mwake.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

36 Hadadi atamwalira, Samila wochokera ku Masireka, analowa ufumu mʼmalo mwake.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 36:36
3 Mawu Ofanana  

Ndipo Husamu anamwalira, ndipo Hadadi mwana wamwamuna wa Bedadi, amene anakantha Midiyani m'dambo la Mowabu, analamulira m'malo mwake: dzina la mzinda wake ndi Aviti.


Ndipo Samila anamwalira, ndipo Shaulo wa ku Rehoboti pambali pa nyanja analamulira m'malo mwake.


Namwalira Hadadi; ndi Samila wa ku Masireka anakhala mfumu m'malo mwake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa