Genesis 36:32 - Buku Lopatulika32 Ndipo Bela mwana wamwamuna wa Beori, analamulira mu Edomu, ndipo dzina la mzinda wake ndilo Dinihaba. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201432 Ndipo Bela mwana wamwamuna wa Beori, analamulira m'Edomu, ndipo dzina la mudzi wake ndilo Dinihaba. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa32 Bela mwana wa Beori, ankalamulira dziko la Edomu, ndipo dzina la mzinda wake linali Dinihaba. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero32 Bela mwana wa Beori anakhala mfumu ya ku Edomu. Mzinda wake ankawutcha Dinihaba. Onani mutuwo |