Genesis 36:30 - Buku Lopatulika30 mfumu Disoni, mfumu Ezere, mfumu Disani; amenewa ndi mafumu obadwa kwa Ahori, monga mwa maufumu ao m'dziko la Seiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 mfumu Disoni, mfumu Ezere, mfumu Disani; amenewa ndi mafumu obadwa kwa Ahori, monga mwa maufumu ao m'dziko la Seiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Disoni, Ezere ndi Disani. Ameneŵa ndiwo mafumu a Ahori m'dziko la Seiri malinga ndi mafuko ao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Disoni, Ezeri ndi Disani. Amenewa ndiwo mafumu a Ahori, monga mwa mafuko awo, mʼdziko la Seiri. Onani mutuwo |