Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Genesis 36:27 - Buku Lopatulika

27 Ana a Ezere ndi awa: Bilihani, ndi Zaavani, ndi Akani.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

27 Ana a Ezere ndi awa: Bilihani, ndi Zaavani, ndi Akani.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

27 Ana a Ezere ndi aŵa: Bilihani, Zaavani ndi Akani.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

27 Ana aamuna a Ezeri anali awa: Bilihani, Zaavani ndi Akani.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 36:27
7 Mawu Ofanana  

ndi Disoni ndi Ezere ndi Disani; amenewa ndi mafumu obadwa kwa Ahori, ana a Seiri, m'dziko la Edomu.


Ana a Disoni ndi awa: Hemudani ndi Esibani ndi Itirani, ndi Kerani.


Ana a Disani ndi awa: Uzi ndi Arani.


Ndi ana a Seiri: Lotani, ndi Sobala, ndi Zibiyoni, ndi Ana, ndi Disoni, ndi Ezere, ndi Disani.


Ana a Ezere: Bilihani, ndi Zaavani, ndi Yaakani. Ana a Disani: Uzi, ndi Arani.


Nachokera ku Meseroti, nayenda namanga mu Bene-Yaakani.


Nachokera ku Bene-Yaakani, nayenda namanga mu Hori Hagidigadi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa