Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Genesis 36:25 - Buku Lopatulika

25 Ana a Ana ndi awa: Disoni ndi Oholibama mwana wamkazi wa Ana.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

25 Ana a Ana ndi awa: Disoni ndi Oholibama mwana wamkazi wa Ana.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

25 Ana a Ana ndi aŵa: Disoni mwana wake wamwamuna, ndi Oholibama mwana wake wamkazi,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

25 Ana a Ana anali: Disoni ndi Oholibama mwana wake wamkazi.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 36:25
7 Mawu Ofanana  

Ana aamuna a Oholibama mwana wamkazi wa Ana, mwana wamkazi wa Zibiyoni, mkazi wake wa Esau, ndi awa: ndipo iye anambalira Esau Yeusi, ndi Yalamu, ndi Kora.


Amenewa ndi ana aamuna a Oholibama mkazi wake wa Esau; mfumu Yeusi, mfumu Yalamu, mfumu Kora, amenewa ndi mafumu obadwa kwa Oholibama mwana wamkazi wa Ana, mkazi wake wa Esau.


Esau anatenga akazi ake a ana aakazi a mu Kanani: Ada mwana wamkazi wa Eloni Muhiti, ndi Oholibama mwana wamkazi wa Ana, mwana wamkazi wa Zibiyoni Muhivi;


Ana a Zibiyoni ndi amenewa: Aiya ndi Ana; ameneyo ndiye Ana uja anapeza akasupe a madzi amoto m'chipululu, pakudyetsa abulu a Zibiyoni atate wake.


Ana a Disoni ndi awa: Hemudani ndi Esibani ndi Itirani, ndi Kerani.


ndipo Oholibama anabala Yeusi, ndi Yalamu, ndi Kora; amenewa ndi ana aamuna a Esau, amene anambadwira m'dziko la Kanani.


Mwana wa Ana: Disoni. Ndi ana a Disoni: Hamurani, ndi Esibani, ndi Itirani, ndi Kerani.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa