Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Genesis 36:20 - Buku Lopatulika

20 Amenewa ndi ana aamuna a Seiri Muhori, okhala m'dzikomo: Lotani ndi Sobala, ndi Zibiyoni, ndi Ana,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

20 Amenewa ndi ana amuna a Seiri Muhori, okhala m'dzikomo: Lotani ndi Sobala, ndi Zibiyoni, ndi Ana,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

20 Aŵa ndi ana aamuna a Seiri Muhori, nzika za dzikolo: Lotani, Sobali, Zibiyoni ndi Ana,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

20 Awa ndi ana a Seiri Mhori, amene ankakhala mʼdzikomo: Lotani, Sobala, Zibeoni, Ana,

Onani mutuwo Koperani




Genesis 36:20
8 Mawu Ofanana  

ndi Ahori paphiri lao Seiri kufikira ku Eliparani, kumene kuli m'mbali mwa chipululu.


Amenewa ndi ana aamuna a Esau, amenewa ndi mafumu ao; yemweyo ndi Edomu.


Esau anatenga akazi ake a ana aakazi a mu Kanani: Ada mwana wamkazi wa Eloni Muhiti, ndi Oholibama mwana wamkazi wa Ana, mwana wamkazi wa Zibiyoni Muhivi;


ndi Disoni ndi Ezere ndi Disani; amenewa ndi mafumu obadwa kwa Ahori, ana a Seiri, m'dziko la Edomu.


Ndipo Ahori anakhala mu Seiri kale, koma ana a Esau analanda dziko lao, nawaononga pamaso pao, nakhala m'malo mwao; monga Israele anachitira dziko lakelake, limene Yehova anampatsa).


monga Iye anachitira ana a Esau, akukhala mu Seiri, pamene anaononga Ahori pamaso pao; ndipo analanda dziko lao, nakhala m'malo mwao kufikira lero lomwe.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa