Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Genesis 36:19 - Buku Lopatulika

19 Amenewa ndi ana aamuna a Esau, amenewa ndi mafumu ao; yemweyo ndi Edomu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

19 Amenewa ndi ana amuna a Esau, amenewa ndi mafumu ao; yemweyo ndi Edomu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

19 Ameneŵa ndi zidzukulu zake za Esau, ndiponso ndiwo mafumu ao.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

19 Amenewa ndiwo zidzukulu za Esau (amene ndi Edomu) ndiponso mafumu awo.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 36:19
5 Mawu Ofanana  

ndipo Esau anati kwa Yakobo, Undipatse ndidye chofiiracho; chifukwa ndalefuka: chifukwa chake anamutcha dzina lake Edomu.


Amenewa ndi ana aamuna a Oholibama mkazi wake wa Esau; mfumu Yeusi, mfumu Yalamu, mfumu Kora, amenewa ndi mafumu obadwa kwa Oholibama mwana wamkazi wa Ana, mkazi wake wa Esau.


Amenewa ndi ana aamuna a Seiri Muhori, okhala m'dzikomo: Lotani ndi Sobala, ndi Zibiyoni, ndi Ana,


Ndipo Esau anakhala m'phiri la Seiri; Esau ndiye Edomu.


Ndipo pamene Saulo atakhazikitsa ufumu wa pa Israele, iye anaponyana ndi adani ake onse pozungulira ponse, ndi Mowabu, ndi ana a Amoni, ndi Edomu ndi mafumu a Zoba, ndi Afilisti; ndipo paliponse anapotolokerapo, anawalanga.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa