Genesis 35:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo Mulungu anati kwa iye, Dzina lako ndi Yakobo; dzina lako silidzatchedwanso Yakobo, koma dzina lako lidzakhala Israele: ndipo anamutcha dzina lake Israele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo Mulungu anati kwa iye, Dzina lako ndi Yakobo; dzina lako silidzatchedwanso Yakobo, koma dzina lako lidzakhala Israele: ndipo anamutcha dzina lake Israele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Mulungu adati, “Dzina lako ndiwe Yakobe, koma kuyambira tsopano, dzina lako lidzakhala Israele.” Motero adayamba kutchedwa Israele. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Mulungu anati kwa iye, “Dzina lako ndiwe Yakobo, koma sudzatchedwanso Yakobo; koma udzatchedwa Israeli.” Choncho anamutcha iye Israeli. Onani mutuwo |