Genesis 34:29 - Buku Lopatulika29 ndi chuma chao chonse ndi ana ao ndi akazi ao anawagwira, nafunkha zonse za m'nyumba. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 ndi chuma chao chonse ndi ana ao ndi akazi ao anawagwira, nafunkha zonse za m'nyumba. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 Adatenga chuma chonse, nagwira akazi onse ndi ana, nkutenganso zonse za m'nyumba mwao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Anawatengera chuma chawo chonse, akazi ndi ana awo, pamodzi ndi zonse zimene zinapezeka mʼnyumba zawo. Zonsezi zinayesedwa ngati zolandidwa ku nkhondo. Onani mutuwo |