Genesis 34:28 - Buku Lopatulika28 Ndipo analanda nkhosa zao ndi zoweta zao ndi abulu ao, ndi za m'mzinda, ndi za m'munda; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 Ndipo analanda nkhosa zao ndi zoweta zao ndi abulu ao, ndi za m'mudzi, ndi za m'munda; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 Adalanda nkhosa, zoŵeta, pamodzi ndi abulu ao ndi zonse zimene zinali mumzindamo ndiponso za ku minda yao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 Analanda nkhosa zawo, ngʼombe zawo, abulu awo ndi china chilichonse chawo mu mzindamo pamodzi ndi za ku minda. Onani mutuwo |