Genesis 31:47 - Buku Lopatulika47 Ndipo Labani anatcha pamenepo Yegara-Sahaduta; koma Yakobo anatcha Galedi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201447 Ndipo Labani anatcha pamenepo Yegara-Sahaduta; koma Yakobo anatcha Galedi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa47 Tsono muluwo Labani adautcha Yagara-Sahaduta, koma mulu womwewo Yakobe adautcha Galedi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero47 Labani anawutcha muluwo Yegara-sahaduta, ndipo Yakobo anawutcha Galeeda. Onani mutuwo |