Genesis 31:36 - Buku Lopatulika36 Ndipo anakwiya Yakobo namkalipira Labani: ndipo Yakobo anayankha nati kwa Labani, Kodi ndachimwa chiyani? Uchimo wanga nguti, kuti unanditsatatsata ine pambuyo panga? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201436 Ndipo anakwiya Yakobo namkalipira Labani: ndipo Yakobo anayankha nati kwa Labani, Kodi ndachimwa chiyani? Uchimo wanga nguti, kuti unanditsatatsata ine pambuyo panga? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa36 Apo Yakobe adapsa mtima kwambiri ndipo adalankhula ndi Labani mokalipa, adati, “Kodi ndakulakwirani chiyani? Kodi ndaphwanya lamulo lotani, kuti mundilondole? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero36 Yakobo anapsa mtima nafunsa Labani mwaukali kuti, “Kodi ndalakwa chiyani? Ndi tchimo lanji limene ndachita kuti muchite kundisaka chonchi? Onani mutuwo |