Genesis 31:31 - Buku Lopatulika31 Ndipo anayankha Yakobo nati kwa Labani, Chifukwa ndinaopa: chifukwa kuti, ndinati, Kapena udzandilanda ine ana ako aakazi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Ndipo anayankha Yakobo nati kwa Labani, Chifukwa ndinaopa: chifukwa kuti, ndinati, Kapena udzandilanda ine ana ako akazi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 Yakobe adayankha kuti, “Ndinkaopa, chifukwa ndinkaganiza kuti mundilanda ana anuŵa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 Yakobo anayankha Labani kuti, “Ine ndinkaopa chifukwa ndinkaganiza kuti mukhoza kundilanda anawa. Onani mutuwo |