Genesis 31:25 - Buku Lopatulika25 Ndipo Labani anakomana naye Yakobo. Ndipo Yakobo anamanga hema wake m'phirimo: ndipo Labani ndi abale ake anamanga m'phiri la Giliyadi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Ndipo Labani anakomana naye Yakobo. Ndipo Yakobo anamanga hema wake m'phirimo: ndipo Labani ndi abale ake anamanga m'phiri la Giliyadi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Labani adampeza Yakobe atamanga mahema kumapiriko. Nayenso Labaniyo adamanga mahema ake komweko ku dziko lamapiri la Giliyadi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Pamene Labani amamupeza Yakobo, nʼkuti Yakobo atamanga matenti ake ku mapiri a dziko la Giliyadi. Nayenso Labani ndi abale ake anamanga matenti awo komweko. Onani mutuwo |